9 Copereka mucipereke kwa Yehova cikhale ca mabango zikwi makumi awiri mphambu zisanu m'litali mwace, ndi zikwi khumi kupingasa kwace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 48
Onani Ezekieli 48:9 nkhani