Ezekieli 5:10 BL92

10 Cifukwa cace atate adzadya ana pakati pako, ndi ana adzadya atate ao; ndipo ndidzacita maweruzo mwa iwe, ndi akutsala onse ndidzawabalalitsa ku mphepo zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:10 nkhani