Ezekieli 5:15 BL92

15 Momwemo cidzakhala cotonza ndi mnyozo, cilangizo ndi codabwiza kwa amitundu akukuzinga, pamene ndikucitira maweruzo mu mkwiyo ndi ukali ndi madzudzulo aukali; Ine Yehovandanena.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:15 nkhani