Ezekieli 5:4 BL92

4 Nutengekonso pa amenewa ndi kuwaponya pakati pa moto, ndi kuwatentha m'moto; kucokera kumeneko udzaturuka moto pa nyumba yonse ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:4 nkhani