Ezekieli 6:4 BL92

4 Ndi maguwa anu a nsembe adzakhala opasuka, ndi zoimiritsa zanu zadzuwa zidzasweka; ndipo ndidzagwetsa ophedwa anu pamaso pa mafano anu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6

Onani Ezekieli 6:4 nkhani