Ezekieli 7:2 BL92

2 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, atero Ambuye Yehova kwa dziko la Israyeli, Kwatha; kwafika kutha kwace pa ngondya zinai za dziko.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:2 nkhani