Ezekieli 7:24 BL92

24 Cifukwa cace ndidzabwera nao amitundu oipitsitsa, ndipo iwo adzalandira nyumba zao ngati colowa, ndidzaleketsanso kudzikuza kwa amphamvu, kuti adetsedwe malo ao opatulika.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:24 nkhani