Ezekieli 7:4 BL92

4 Ndipo diso langa silidzakulekerera, sindidzacita cifundo, koma ndidzakubwezera njira zako, ndi zonyansa zako zidzakhala pakati pako; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 7

Onani Ezekieli 7:4 nkhani