Ezekieli 8:14 BL92

14 Pamenepo anadza nane ku citseko ca cipata ca nyumba ya Yehova coloza kumpoto; ndipo taonani, apo panakhala akazi akulirira Tainuzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 8

Onani Ezekieli 8:14 nkhani