7 Ndi ana amuna a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Raama, ndi Sabiteka; ndi ana a Raama: Sheba ndi Dedane.
Werengani mutu wathunthu Genesis 10
Onani Genesis 10:7 nkhani