Genesis 11:3 BL92

3 Ndipo ananenana wina ndi wina, Tiyeni tipange njerwa, tiziocetse. Ndipo anali ndi njerwa naziyesa miyala, ndi katondo anayesa matope.

Werengani mutu wathunthu Genesis 11

Onani Genesis 11:3 nkhani