Genesis 11:4 BL92

4 Ndipo anati, Tiyeni, timange mudzi ndi nsanja, pamutu pace pafikire kumwamba; ndipo tidzipangire ife tokha dzina kuti tisabalalike pa dziko lonse lapansi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 11

Onani Genesis 11:4 nkhani