15 Ndipo akaronga ace a Farao anamuona iye, namyamikira iye kwa Farao; ndipo anamuka ndi mkazi kunyumba kwace kwa Farao.
Werengani mutu wathunthu Genesis 12
Onani Genesis 12:15 nkhani