Genesis 14:22 BL92

22 Ndipo Abramu anati kwa mfumu ya Sodomu, Dzanja langa ndamtukulira Yehova, Mulungu Wamkurukuru, mwini kumwamba ndi dziko lapansi,

Werengani mutu wathunthu Genesis 14

Onani Genesis 14:22 nkhani