23 kuti sindidzatenga ngakhale thonje ngakhale cingwe ca nsapato, ngakhale kanthu kali konse kako, kuti unganene, Ndamlemeza Abramu;
Werengani mutu wathunthu Genesis 14
Onani Genesis 14:23 nkhani