Genesis 18:32 BL92

32 Ndipo anati, Asakwiyetu Ambuye, ndipo ndidzanena kamodzi aka kokha: kapena akapezedwakhumim'menemo: Ndipo anati, Sindidzacita cifukwa ca khumi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 18

Onani Genesis 18:32 nkhani