32 Munthuyo ndipo analowa m'nyumba, namasula ngamila, napatsa ngamila maudzu ndi cakudya, ndi madzi akusamba mapazi ace ndi mapazi a iwo amene anali naye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 24
Onani Genesis 24:32 nkhani