5 Ndipo anati kwa iye mnyamatayo, Kapena sadzafuna mkaziyo kunditsata ine ku dziko lino: kodi ndikambwezerenso mwana wanu kudziko komwe mwacokera inu?
Werengani mutu wathunthu Genesis 24
Onani Genesis 24:5 nkhani