Genesis 26:12 BL92

12 Ndipo Isake anabzala m'dzikomo, nalandira za makumi khumi caka cimeneco; ndipo Yehova anamdalitsa iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:12 nkhani