Genesis 27:18 BL92

18 Ndipo iye analowa kwa atate wace, nati, Atate wanga; iye anati, Ndine pano; ndani iwe mwana wanga?

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:18 nkhani