30 Ndipo panali atatha Isake kumdalitsa Yakobo, ataturuka Yakobo pamaso pa Isake atate wace, Esau mkuru wace analowa kucokera kuthengo,
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:30 nkhani