31 Ndipo iyenso anakonza cakudya cokolera, nadza naco kwa atate wace, nati kwa atate wace, Auke atate wanga, adye nyama ya mwana wace, kuti moyo wanu undidalitse ine.
Werengani mutu wathunthu Genesis 27
Onani Genesis 27:31 nkhani