Genesis 27:32 BL92

32 Ndipo Isake atate wace anati kwa iye, Ndiwe yani? ndipo iye anati, Ndine mwana wanu woyamba Esau.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:32 nkhani