3 Ndipo Rakele anati, Taonani mdzakazi wanga Biliha, mulowe kwa iye; ndipo iye adzabala pa maondo anga, kuti inenso ndionerepo ana pa iye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 30
Onani Genesis 30:3 nkhani