Genesis 30:4 BL92

4 Ndipo Rakele anampatsa iye Biliha mdzakazi wace akhale mkazi wace; ndipo Yakobo analowa kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:4 nkhani