6 Rakele ndipo anati, Mulungu wandiweruzira ine, namva mau anga, nandipatsa ine mwana; cifukwa cace anamucha dzina lace Dani.
Werengani mutu wathunthu Genesis 30
Onani Genesis 30:6 nkhani