Genesis 32:26 BL92

26 Ndipo iye anati Ndileke ndimuke, cifukwa kulinkuca. Ndipo Yakobo anati, Sindidzakuleka iwe kuti umuke, ukapanda kundidalitsa ine.

Werengani mutu wathunthu Genesis 32

Onani Genesis 32:26 nkhani