28 Ndipo anati, Dzina lako silidzachedwanso Yakobo, koma Israyeli, cifukwa unayesana naye Mulungu ndithu, ndipo unapambana.
Werengani mutu wathunthu Genesis 32
Onani Genesis 32:28 nkhani