29 Yakobo ndipo anafunsa iye, nati, Undiuze ine dzina lako. Ndipo iye anati, Undifunsa dzina cifukwa ninji? Ndipo anamdalitsa iye pamenepo.
Werengani mutu wathunthu Genesis 32
Onani Genesis 32:29 nkhani