Genesis 33:13 BL92

13 Ndipo anati kwa iye, Mbuyanga adziwa kuti ana ali ambowa, ndipo nkhosa ndi zoweta ndiri nazo zirinkuyamwitsa: ndipo akathamangitsa tsiku limodzi zoweta zonse zidzafa.

Werengani mutu wathunthu Genesis 33

Onani Genesis 33:13 nkhani