14 Mbuyanga atsogoleretu kapolo wace, ndipo ine ndidzazitsogolera pango'no-pang'ono monga mwa mayendedwe a zoweta ziri pamaso panga, ndi monga mwa mayendedwe a ana, mpaka ndifike kwa mbuyanga ku Seiri.
Werengani mutu wathunthu Genesis 33
Onani Genesis 33:14 nkhani