4 Ndipo Esau anathamangira kukomana naye namfungatira, nagwa pankhope pace, nampsompsona; ndipo analira iwo.
Werengani mutu wathunthu Genesis 33
Onani Genesis 33:4 nkhani