Genesis 33:5 BL92

5 Ndipo anatukula maso ace nawaona akazi ndi ana; nati, Ndani awa ali ndi iwe? Ndipo iye anati, Ndiwo ana amene Mulungu anakomera mtima kumpatsa kapolo wanu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 33

Onani Genesis 33:5 nkhani