Genesis 36:33 BL92

33 Ndipo Bela anamwalira, ndipo Jobabi mwana wamwamuna wa Zera wa ku Bozara analamulira m'malomwace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36

Onani Genesis 36:33 nkhani