Genesis 44:1 BL92

1 Ndipo Yosefe anauza tsanyumba wace kuti, Dzaza matumba a anthuwo ndi cakudya, monga angathe kunyamula, ndi kuika ndalama za yense kukamwa kwa thumba lace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:1 nkhani