13 Ndipo mudzafotokozera atate wanga za ulemerero wanga wonse m'Aigupto, ndi zonse mwaziona; ndipo muzifulumira ndi kutsitsira kuno atate wanga.
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:13 nkhani