16 Ndipo mbiri yace inamveka m'nyumba ya Farao, kuti abale ace a Yosefe afika; ndipo inamkomera Farao, ndi anyamata ace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:16 nkhani