17 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Nena ndi abale ako, Citani ici; senzetsani nyama zanu, ndi kupita kunka ku dziko la Kanani;
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:17 nkhani