21 Ndipo ana a Israyeli anacita cotero: ndipo Yosefe anawapatsa iwo magareta monga analamulira Farao, nawapatsa phoso la panjira,
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:21 nkhani