22 Onse anawapatsa yense zobvala zopindula; koma Benjamini anampatsa ndalama zasiliva mazana atatu ndi zobvala zopindula zisanu.
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:22 nkhani