28 Ndipo anatumiza Yuda patsogolo pace kwa Yosefe, amtsogolere kumuonetsa njira yomka ku Goseni: ndipo anafika ku dziko la Goseni.
Werengani mutu wathunthu Genesis 46
Onani Genesis 46:28 nkhani