21 Ndipo Israyeli anati kwa Yosefe, Taona, ndirinkufa ine; Mulungu adzakhala ndi iwe, adzakubwezanso iwe ku dziko la makolo ako.
Werengani mutu wathunthu Genesis 48
Onani Genesis 48:21 nkhani