31 pamenepo anaika Abrahamu ndi Sara mkazi wace; pamenepo anaika Isake ndi Rebeka mkazi wace: pamenepo ndinaika Leya:
Werengani mutu wathunthu Genesis 49
Onani Genesis 49:31 nkhani