Genesis 7:15 BL92

15 Ndipo zinalowa kwa Nowa m'cingalawamo ziwiri ziwiri zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 7

Onani Genesis 7:15 nkhani