16 Zimene zinalowazo, zinalowa yamphongo ndi yaikazi zamoyo zonse, monga momwe Mulungu anamlamulira iye: ndipo Yehova anamtsekera iye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 7
Onani Genesis 7:16 nkhani