17 Ndipo cigumula cinali pa dziko lapansi masiku makumi anai: ndipo madzi anacuruka natukula cingalawa, ndipo cinakwera pamwamba pa dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu Genesis 7
Onani Genesis 7:17 nkhani