Genesis 8:22 BL92

22 Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, cisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.

Werengani mutu wathunthu Genesis 8

Onani Genesis 8:22 nkhani