1 Ndipo Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ace, nati kwa iwo, Mubalane, mucuruke, mudzaze dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu Genesis 9
Onani Genesis 9:1 nkhani