11 Ndi nkhope zao ndi mapiko ao zinagawikana kumutu; ciri conse cinali nao mapiko awiri olumikizana, ndi awiri anaphimba thupi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:11 nkhani