12 Ndipo zinayenda, ciri conse cinalunjika kutsogolo kwace uko mzimu unafuna kumukako zinamuka, sizinatembenuka poyenda.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:12 nkhani